Job 19:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu odzacheza kunyumba kwanga andiiŵala, Antchito anga nawonso sakundilemekeza, ndasanduka ngati wakudza m'maso mwao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo a m'nyumba mwanga ndi adzakazi anga andiyesa mlendo; ndine wachilendo pamaso pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu odzacheza ku nyumba kwanga ndiponso antchito anga aakazi andisandutsa mlendo; ndasanduka mlendo mʼmaso mwawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo a m'nyumba mwanga ndi adzakazi anga andiyesa mlendo; Ndine wacilendo pamaso pao.