Job 19:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikaitana wantchito, sandiyankha, ndimachita kupemba kuti andichitire kanthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikaitana kapolo wanga, sandibwezera mau, chinkana ndimpembedza pakamwa panga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikayitana wa ntchito wanga, iye sandiyankha, ngakhale ndikapempha ndi pakamwa panga sandichitira kanthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikaitana kapolo wanga, sandibwezera mau, Cinkana ndimpembedza pakamwa panga.