Job 19:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale ana omwe amandinyoza, ndikamayenda amandinyodola.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Angakhale ana ang'ono andipeputsa, ndikanyamuka, andinena;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inde, ngakhale ana amandinyoza; akandiona amandinyodola.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Angakhale ana ang'ono andipeputsa, Ndikanyamuka, andinena;