Job 19:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Kodi mudzakhala mukundizunzabe mpaka liti? Chifukwa chiyani mukundilasa ndi mau anu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzasautsa moyo wanga kufikira liti, ndi kundithyolathyola nao mau?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi mudzakhala mukundizunza mpaka liti, ndi kundilasa ndi mawu anuwo?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzasautsa moyo wanga kufikira liti, Ndi kundityolatyola nao mau?