Job 19:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndangoti gwa kuwonda, moyo wanga wapulumukira pang'onong'ono.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Fupa langa laumirira pa khungu langa ndi mnofu wanga, ndipo ndapulumuka ndili nazo nkhama za mano anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndangotsala khungu ndi mafupa okhaokha; ndapulumuka lokumbakumba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pfupa langa laumirira pa khungu langa ndi mnofu wanga, Ndipo ndapulumuka ndiri nazo nkhama za mano anga.