Job 19:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ha, achikhala ena adaakumbukira mau anga! Ha, achikhala mauwo adaalembedwa m'buku!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ha! Akadalembedwa mau anga! Ha! Akadalembedwa m'buku!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Aa, achikhala mawu anga analembedwa, achikhala analembedwa mʼbuku,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ha! akadalembedwa mau anga! Ha! akadalembedwa m'buku!