Job 19:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndemwe ndidzamuwona, osati winanso ai. Ndidzamuwona ndi maso angaŵa. Mtima wanga ukulifunitsitsa tsikulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene ndidzampenya ndekha, ndi maso anga adzamuona, si wina ai. Imso zanga zatha m'kati mwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndemwe ndidzamuona Iye ndi maso angawa, ineyo, osati wina ayi. Ndithu mtima wanga ukufunitsitsadi!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amene ndidzampenya ndekha, Ndi maso anga adzamuona, si wina ai. Imso zanga zatha m'kati mwanga.