Job 19:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma inu mukuti, ‘Ha, tingamzunze bwanji, popeza kuti zovuta zonsezi zaoneka chifukwa cha iye yemweyo?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mukati, Tiyeni timlondole! Popeza chifukwa cha mlandu chapezeka mwa ine;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma inu mukuti, ‘Haa! Tingamuzunze bwanji, popeza kuti zonsezi zaoneka chifukwa cha iye yemweyo?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mukati, Tiyeni timlondole! Popeza cifukwa ca mlandu capezeka mwa ine;