Job 19:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu muwope chilango, chifukwa ukali wa Mulungu umalangadi mosalephera. Motero mudzadziŵa kuti chiweruzo chilipo ndithu.” Zofari
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
muchite nalo mantha lupanga; pakuti mkwiyo utenga zolakwa za lupanga, kuti mudziwe pali chiweruzo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu muyenera kuopa lupanga; pakuti mkwiyo wake umalangadi ndi lupanga; zikadzatero muzadziwa kuti chiweruzo chilipo ndithu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mucite nalo mantha lupanga; Pakuti mkwiyo utenga zolakwa za lupanga, Kuti mudziwe pali ciweruzo.