Job 19:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwakhala mukundinyoza kambirimbiri, Bwanji osachita manyazi kuti mukundisautsa?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kakhumi aka mwandichititsa manyazi; mulibe manyazi kuti mundiumira mtima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inuyo mwandinyoza kwambiri; mwanditsutsa mopanda manyazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kakumi aka mwandicititsa manyazi; Mulibe manyazi kuti mundiumira mtima.