Job 19:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale zitakhala zoona kuti ndachimwa, kuchimwakotu nkwanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ngati ndalakwa ndithu, kulakwa kwanga kuli ndi ine ndekha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati ndi zoona kuti ine ndasochera, cholakwachotu nʼchanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ngati ndalakwa ndithu, Kulakwa kwanga kuli ndi ine ndekha.