Job 19:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithudi, mukuganiza kuti mukundipambana. Mukuti mavuto angaŵa akusonyeza kuchimwa kwanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati inu mudzikuza ndithu pa ine, ndi kunditchulira mtonzo wanga kuti munditsutse nao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati ndithudi mukudziyika nokha pamwamba panga, ndi kugwiritsa ntchito kunyozedwa kwanga polimbana nane,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati inu mudzikuza ndithu pa ine, Ndi kundichulira mtonzo wanga kuti munditsutse nao;