Job 19:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma tsono mudziwe kuti Mulungu ndiye wandichita zimenezi, ndiye amene wanditchera msampha umenewu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dziwani tsopano kuti Mulungu wandikhotetsera mlandu wanga, nandizinga ndi ukonde wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pamenepa dziwani kuti Mulungu wandilakwira ndipo wandizinga ukonde wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dziwani tsopano kuti Mulungu wandikhotetsera mlandu wanga, Nandizinga ndi ukonde wace.