Job 19:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithu, ndimafuula kuti, ‘Mayo, akundizunza ine!’ Koma palibe wondiyankha. Ndimapempha chithandizo, koma palibe wondichitira zolungama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, ndifuula kuti, Chiwawa! Koma sandimvera; ndikuwa, koma palibe chiweruzo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngakhale ndifuwule kuti, ‘Akundizunza!’ Palibe wondiyankha; ngakhale ndipemphe thandizo, palibe wondichitira zolungama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, ndipfuula kuti, Ciwawa! koma sandimvera; Ndikuwa, koma palibe ciweruzo.