Job 19:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mulungu wanditsekera njira, kotero kuti sindingathe kubzola. Njira yangayo waiphimba ndi mdima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye ananditsekera njira kuti ndisapitireko, naika mdima poyendapo ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu wanditsekera njira yanga kotero sindingathe kudutsa; waphimba njira zanga ndi mdima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye ananditsekera njira kuti ndisapitireko, Naika mdima poyendapo ine.