Job 19:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye wandilanda ulemerero wanga, wandivula chisoti chaulemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anandivula ulemerero wanga, nandichotsera korona pamutu panga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye wandilanda ulemu wanga ndipo wandivula chipewa chaufumu pamutu panga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anandibvula ulemerero wanga, Nandicotsera korona pamutu panga,