Job 2:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ataona Yobeyo chakutali, sadamzindikire, ndipo adayamba kulira mofuula. Adang'amba zovala zao, nadzithira fumbi kumutu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pokweza maso ao ali kutali, sanamdziwe, nakweza mau ao, nalira; nang'amba yense malaya ake, nawaza fumbi kumwamba ligwe pamitu pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atamuona Yobuyo, iwo ali chapatalipo, sanathe kumuzindikira. Choncho anayamba kulira mokweza mawu ndipo anangʼamba mikanjo yawo ndi kuwaza fumbi pa mitu yawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pokweza maso ao ali kutali, sanamdziwa, nakweza mau ao, nalira; nang'amba yense maraya ace, nawaza pfumbi kumwamba ligwe pamitu pao.