Job 2:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Satana adayankha kuti, “Koma ayesedwe m'thupi mwake. Zinthu zonse zimene munthu ali nazo angathe kuzipereka, chikulu iyeyo ali moyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nayankha Satana, nati kwa Yehova, Khungu kulipa khungu, inde munthu adzapereka zonse ali nazo kuombola moyo wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Satana anayankha kuti, “Iye ayesedwe mʼthupi mwake. Munthu angathe kupereka zonse ali nazo malingana iyeyo ali ndi moyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nayankha Satana, nati kwa Yehoya, Khungu kulipa khungu, inde munthu adzapereka zonse ali nazo kuombola moyo wace.