Job 2:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma tsopano taonongani thupi lake, muwona, adzakutukwanirani pamaso.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma tambasulani dzanja lanu, ndi kukhudza fupa lake ndi mnofu wake, ndipo adzakuchitirani mwano pamaso panu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma tatambasulani dzanja lanu ndi kuwononga thupi lake, ndipo iyeyo adzakutukwanani ndithu pamaso panu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma tambasulani dzanja lanu, ndi kukhudza pfupa lace ndi mnofu wace, ndipo adzakucitirani mwano pamaso panu.