Job 2:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adauza Satana uja kuti, “Chabwino, iyeyo uchite naye zonse zimene ukufuna, koma moyo wake wokha usauchotse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anati kwa Satana, Taona, akhale m'dzanja lako; moyo wake wokha uuleke.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anati kwa Satana, “Chabwino, iye ali mʼmanja mwako; koma moyo wake usawuchotse.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anati kwa Satana. Taona, akhale m'dzanja lako; moyo wace wokha uuleke.