Job 2:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mkazi wake adamuuza kuti, “Ha! Mukukhalabe okhulupirika motere! Ingomtukwanani Mulunguyo, mufe basi!”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mkazi wake ananena naye, Kodi uumiriranso kukhala wangwiro? Chitira Mulungu mwano, ufe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkazi wake anati kwa iye, “Kodi ukuwumirirabe kukhala wangwiro? Tukwana Mulungu kuti ufe!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mkazi wace ananena naye, Kodi uumiriranso kukhala wangwiro? citira Mulungu mwano, ufe.