Job 20:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Thupi lake ndi la nyonga zaunyamata, komabe nyongazo zidzatha naye limodzi m'fumbi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mafupa ake adzala nao unyamata wake, koma udzagona naye pansi m'fumbi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mphamvu zaunyamata zimene zili mʼthupi mwake zidzagona naye limodzi mʼfumbi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mafupa ace adzala nao unyamata wace, Koma udzagona naye pansi m'pfumbi.