Job 20:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Zoipa zimakhala zozuna kwa iye, nchifukwa chake amachita ngati kuzisunga m'kamwa mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chinkana choipa chizuna m'kamwa mwake, chinkana achibisa pansi pa lilime lake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngakhale zoyipa zili zozuna mʼkamwa mwake ndipo amazibisa kunsi kwa lilime lake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cinkana coipa cizuna m'kamwa mwace, Cinkana acibisa pansi pa lilime lace;