Job 20:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale safuna kuleka kuzivumata, nangozisunga m'kamwa mwakemo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chinkana achisunga, osachileka, nachikhalitsa m'kamwa mwake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngakhale salola kuzilavula, ndipo amazisunga mʼkamwa mwake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cinkana acisunga, osacileka, Naoikhalitsa m'kamwa mwace;