Job 20:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
zoipazo akazimeza, zimaloŵa m'mimba mwake. Zimasanduka ngati ndulu ya mphiri m'kati mwa iyeyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma chakudya chake chidzasandulika m'matumbo mwake, chidzakhala ndulu ya mphiri m'kati mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
koma chakudya chake chidzawawasa mʼmimba mwake; chidzasanduka ngati ndulu ya njoka mʼkati mwa iyeyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma cakudya cace cidzasandulika m'matumbo mwace, Cidzakhala ndulu ya mphiri mkati mwace.