Job 20:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amapeza chuma, koma amachisanzanso. Mulungu amachitulutsa m'mimba mwa munthuyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anachimeza chuma koma adzachisanzanso; Mulungu adzachitulutsa m'mimba mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adzachisanza chuma chimene anachimeza; Mulungu adzachitulutsa mʼmimba mwa munthuyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anacimeza cuma koma adzacisanzanso; Mulungu adzaciturutsa m'mimba mwace.