Job 20:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimene amadya zili ngati ululu wa mphiri, ndipo ululuwo udzamupha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzayamwa ndulu ya mphiri; pakamwa pa njoka padzamupha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye adzayamwa ndulu ya njoka ndipo ululu wa mphiri udzamupha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzayamwa ndulu ya mphiri; Pakamwa pa njoka padzamupha.