Job 20:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe Yobe, wandipsetsa mtima. Nchifukwa chake ndikufulumira kuyankha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'mwemo zolingirira zanga zindiyankha, chifukwa chake ndifulumidwa m'kati mwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kuvutika kwa mʼmaganizo kwanga kwandifulumiza kuti ndiyankhe chifukwa ndasautsidwa kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'mwemo zolingirira zanga zindiyankha, Cifukwa cace ndifulumidwa m'kati mwanga.