Job 20:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale ndi wachuma, adzakhala mmphaŵi. Mavuto aakulu adzamgwera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pomkwanira kudzala kwake adzakhala m'kusauka; dzanja la yense wovutika lidzamgwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale ndi munthu wachuma, mavuto adzamugwera; mavuto aakulu adzamugwera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pomkwanira kudzala kwace adzakhala m'kusauka; Dzanja la yense wobvutika lidzamgwera,