Job 20:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa nthaŵi yoti adyerere chuma china, Mulungu adzamgwetsera ukali wamoto ngati mvula yosakata.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Poti adzaze mimba yake, Mulungu adzamponyera mkwiyo wake waukali, nadzamvumbitsira uwu pakudya iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akadya nʼkukhuta, Mulungu adzamugwetsera ukali wamoto ngati mvula yosalekeza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Poti adzaze mimba yace, Mulungu adzamponyera mkwiyo wace waukali, Nadzambvumbitsira uwu pakudya iye.