Job 20:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chigumula cha madzi chidzaononga nyumba yake. Katundu wake yense adzachotsedwa pa tsiku la mkwiyo wa Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Phindu la m'nyumba mwake lidzachoka, akatundu ake adzamthawa tsiku la mkwiyo wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chigumula cha madzi chidzawononga nyumba yake, katundu wake adzatengedwa pa tsiku la ukali wa Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Phindu la m'nyumba mwace lidzacoka, Akatundu ace adzamthawa tsiku la mkwiyo wace.