Job 20:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Izi nzimene Mulungu amasungira munthu woipa. Ndizo zimene Mulungu adalamula kuti zikhale mphotho ya munthuyo.” Yobe
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ili ndi gawo la munthu woipa, lochokera kwa Mulungu, ndi cholowa amuikiratu Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Izi ndi zimene Mulungu amasungira anthu oyipa, mphotho imene Mulungu amayikira iwowo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ili ndi gawo la munthu woipa, locokera kwa Mulungu, Ndi colowa amuikiratu Mulungu.