Job 20:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikumva mau ondidzudzula ndi ondinyoza, koma ndadziŵa kale m'mene ndingathe kuyankhira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndamva kudzudzula kwakundichititsa manyazi, ndi mzimu wa nzeru yanga undiyankha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikumva kudzudzula kondinyoza, ndipo kumvetsetsa kwanga kwa zinthu kwandifulumiza kuti ndiyankhe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndamva kudzudzula kwakundicititsa manyazi, Ndi mzimu wa nzeru yanga undiyankha.