Job 20:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi sukudziŵa kuti kukondwera kwa woipa nkosakhalira kutha? Kodi sukudziŵa kuti chimwemwe cha munthu wopanda Mulungu ncha kanthaŵi chabe?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti kufuula kokondwera kwa woipa sikukhalira kutha, ndi chimwemwe cha wonyoza Mulungu chikhala kamphindi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti chisangalalo cha woyipa nʼchosachedwa kutha, chimwemwe cha wosapembedza Mulungu nʼchakanthawi kochepa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti kupfuula kokondwera kwa woipa sikukhalira kutha, Ndi cimwemwe ca wonyoza Mulungu cikhala kamphindi?