Job 20:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale mbiri yake ifalikire ponseponse, ndipo ulemerero wake ukwere kufikira ku mlengalenga,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chinkana ukulu wake ukwera kunka kuthambo, nugunda pamitambo mutu wake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale atamayenda mapewa ake ali mmwamba ndipo mutu wake uli nengʼaa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cinkana ukulu wace ukwera kumka kuthambo, Nugunda pamitambo mutu wace;