Job 20:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
adzatheratu monga momwe imatayikira ndoŵe yake. Amene ankamuwona azidzafunsa kuti, ‘Kodi uje uja ali kuti?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma adzatayika kosatha ngati zonyansa zake; iwo amene adamuona adzati, Ali kuti iye?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
iye adzatheratu monga momwe imatayikira ndowe yake yomwe; iwo amene ankamuona adzati, ‘Kodi uje uja ali kuti?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma adzatayika kosatha ngati zonyansa zace; Iwo amene adamuona adzati, Ali kuti iye?