Job 21:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mumafunsana kuti, ‘Kodi nyumba ya mkulu uja ili kuti? Kodi hema limene munkakhala anthu oipa aja lili kuti?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti munena, Ili kuti nyumba ya kalonga? Ndi hema wokhalamo woipa ali kuti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mukuti, ‘Kodi nyumba ya mkulu uja ili kuti, matenti amene munkakhala anthu oyipa aja ali kuti?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti munena, Iri kuti nyumba ya kalonga? Ndi hema wokhalamo woipa ali kuti?