Job 21:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Palibe ndi mmodzi yemwe amene amadzudzula munthu woipa, kapena kumbwezera zoipa zimene adachita.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzamfotokozera ndani njira yake pamaso pake? Nadzamlipitsa ndani pa ichi anachichita?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ndani amadzudzula munthu wochimwayo? Ndani amamubwezera zoyipa zimene anachita?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzamfotokozera ndani njira yace pamaso pace? Nadzamlipitsa ndani pa ici anacicita?