Job 21:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu onse amatsatira mtembo wake. Amene amatsogola ndi osaŵerengeka, ndipo amakaika mtembo wakewo bwinobwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zibuma za kuchigwa zidzamkomera. Adzakoka anthu onse amtsate, monga anamtsogolera osawerengeka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dothi la ku chigwa limamukomera; anthu onse amatsatira mtembo wake, ndipo anthu osawerengeka amakhala patsogolo pa chitanda chakecho.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zibuma za kucigwa zidzamkomera. Adzakoka anthu onse amtsate, Monga anamtsogolera osawerengeka.