Job 21:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mabanja ao amakhala pabwino opanda mantha, mkwapulo wa Mulungu suŵakhudza nkomwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyumba zao sizitekeseka ndi mantha, ngakhale ndodo ya Mulungu siiwakhalira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mabanja awo amakhala pa mtendere ndipo sakhala ndi mantha; mkwapulo wa Mulungu suwakhudza nʼkomwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nyumba zao sizitekeseka ndi mantha, Ngakhale ndodo ya Mulungu siiwakhalira.