Job 22:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake misamphayi yakuzinga, ndipo wadzidzimuka ndi mantha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake misampha ikuzinga. Ndi mantha akuvuta modzidzimutsa,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake misampha yakuzungulira, nʼchifukwa chake tsoka ladzidzidzi lakuchititsa mantha,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace misampha ikuzinga. Ndi mantha akubvuta modzidzimutsa,