Job 22:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuli mdima ndipo sungathe kuwona kanthu, madzi achigumula akukumiza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kapena mdima kuti ungaone, ndi madzi aunyinji akumiza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
nʼchifukwa chake kuli mdima kuti sungathe kuona kanthu, nʼchifukwa chakenso madzi achigumula akumiza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kapena mdima kuti ungaone, Ndi madzi aunyinji akumiza.