Job 22:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Kodi Mulungu sali kutalitali kumwamba? Ona nyenyezi zili m'mwamba kwambirizo, ona kutalika kwake pamene ziliripo!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi Mulungu sakhala m'mwamba m'tali? Ndipo penyani kutalika kwake kwa nyenyezi, zili m'talitali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi Mulungu sali kutalitali kumwamba? Ndipo ona nyenyezi zili mmwamba kwambirizo, ona kutalika kwake pamene zililipo!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi Mulungu sakhala m'mwamba m'tali? Ndipo penyani kutalika kwace kwa nyenyezi, ziri m'talitali.