Job 22:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe umanena kuti, ‘Kodi Mulungu amadziŵa chiyani? Wabisika ndi mitambo, nanga angatiweruze bwanji?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ukuti, Adziwa chiyani Mulungu? Aweruza kodi mwa mdima wa bii?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe iweyo ukunena kuti, ‘Kodi Mulungu amadziwa chiyani? Kodi Iye amaweruza mu mdima woterewu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ukuti, Adziwa ciani Mulungu? Aweruza kodi mwa mdima wa bii?