Job 22:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chonsecho ndi Mulungu amene adaŵalemeretsa ndi zinthu zokoma. Nchifukwa chake ine ndekha ndiye maganizo a anthu oipa sindigwirizana nawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Angakhale Iye adadzaza nyumba zao ndi zabwino; koma uphungu wa oipa unditalikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chonsecho ndi Iye amene anadzaza nyumba zawo ndi zinthu zabwino, choncho ine sindigwirizana ndi uphungu wa anthu oyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Angakhale Iye adadzaza nyumba zao ndi zabwino; Koma uphungu wa oipa unditalikira.