Job 22:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu abwino amaona zonse ndi kukondwa, anthu osachimwa amangoseka, akamaona oipa akulangidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Olungama achiona nakondwera; ndi osalakwa awaseka pwepwete,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Anthu olungama amaona kuwonongeka kwawo ndipo amakondwera; anthu osalakwa amangoseka, akamuona woyipa akulangidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Olungama aciona nakondwera; Ndi osalakwa awaseka pwepwete,