Job 22:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Golide wako yense umuyese wachabechabe, ndithu, chuma chamtengowapatali uchiwone ngati dothi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo utaye chuma chako kufumbi, ndi golide wa ku Ofiri ku miyala ya kumitsinje.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo chuma chamtengowapatali nuchiona ngati fumbi, golide wa ku Ofiri numutaya ku miyala ya ku zigwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo utaye cuma cako kupfumbi, Ndi golidi wa ku ofiri ku miyala ya kumitsinje.