Job 22:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Mphambe ndiye akhale ngati golide wako, akhale ngati siliva wako wamtengowapatali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Wamphamvuyonse adzakhala chuma chako, ndi ndalama zako zofunika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Wamphamvuzonseyo adzakhala golide wako, siliva wako wamtengowapatali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Wamphamvuyonse adzakhala cuma cako, Ndi ndarama zako zofunika.