Job 22:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chimene wachitsimikiza kuti udzachite, chidzachitikadi, kuŵala kudzakuunikira pa njira zako zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ukatsimikiza mtima kakuti, kadzakhazikikira iwe; ndi kuunika kudzawala pa njira zako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chimene watsimikiza kuti uchite, chidzachitikadi, kuwala kudzakuwunikira pa njira yako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ukatsimikiza mtima kakuti, kadzakhazikikira iwe; Ndi kuunika kudzawala pa njira zako.