Job 22:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pajatu Mulungu amagwetsa onyada, koma amapulumutsa odzichepetsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anthu akakugwetsa pansi, udzati, Adzandikweza; ndipo adzapulumutsa wodzichepetsayo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene anthu agwetsedwa pansi, iwe nʼkunena kuti, ‘Akwezeni!’ Pamenepo Iye adzapulumutsa anthu oponderezedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anthu akakugwetsa pansi, udzati, Adzandikweza; Ndipo adzapulumutsa wodzicepetsayo.